Lyric provided by www.seekalyric.com

Ndili bwino, ndakondwa
Ndikupita ku nyumba
Mudzi uli pafupi

Tsiku lonse, madzulo
Ndili bwino, ndakondwa
Ndikupita ku nyumba
Tauni uli pafupi

Monitu tso-o-no!
Kunyumba kuli bwanji?
Onse ali bwino?